Olemekezeka a Sameer Suleman, akukumbutsa masapota onse a DPP kuti palibe ngakhale modzi amene agwedezeke kapena kubwelera m’mbuyo chifukwa choti chipani cha DPP chili ku opposition.
Chipani chipitilira kukhala cha mphamvu.
Mtendere kapena kuzunzidwa, koma APM komanso masapota a DPP simuli nokha.
Palibe yemwe akugwedezeka.
Palibeso yemwe akuopa.
DPP ilipo ndipo izakhalapo.
Ndi Nkhanimchitumbuka.com simudzakhalanso mu mdima wa chilungamo.
Related Posts
Kumvetsa vuto la kukwera kwa Blood Pressure (BP)
Machinga registers 2,336 teen pregnancies due to school closure
Kusowa magazi pamene muli oyembekezera