Nkhani Mchitumbuka

Malawi News Updates

Covid-19 yikupha pano winanso wa UTM

Kucha kwa lero mkulu wina muchipani cha UTM Alhaji Sande wasendela kumasano mlili wa Covid 19 utamusautsa kwaka nthawi kochepa.

COVID 19 IKUPITILILA KUSAKAZA MIYOYO YA ANTHU MDZIKO LINO CHONDE A MALAWI SAMALANI

Miyoyo ya wanthu mdziko lino maka ya akuluakulu pandale ikupitilila kusakazika ndi mlili wa Covid 19.

Kucha kwa lero mkulu wina muchipani cha UTM Alhaji Sande wasendela kumasano mlili wa Covid 19 utamusausa kwaka nthawi kochepa.

Anthu enaso ochita malonda ndi ena ogwila ntchito zosiyanasiyana asendela kumasano kucha kwa lero kamba ka mlili womwewu wa Covid 19.

Ulendo waku manda

Pali chiyembekezo choti mlili wa Covid 19 usiya kufala nyengo yotentha ikafika.

Chonde a Malawi!!! Ife antolankhani a Malawi News Agency tikukupemphani kuti musiye kuyendayenda mumatawuni a dziko lino kamba mlili wumenewu ndi oophya ndipo simungagule moyo wanu ndi ndalama

Category