Nkhani Mchitumbuka

Malawi News Updates

Cadet wa DPP Davie Chikaonda wapatsidwa belo

Modzi mwa anyamata omwe ndi Masapota a DPP yemwe dzina lake pa Facebook amatchuka kuti Davie Chikaonda lero akuyembekezeleka kutuluka pa belo.
.
Davie Chikaonda yemwe ndi wa Nyekhwe news yemwe nkhani zomwe analemba ndi zotsusana ndi Kongeresi, anamangidwa masiku awiri apitawo pomwe a Kongeresi amumveka mlandu woti wapezeka ndi ma computer osunga zinsinsi za ku state house.
.
Zambiri tikupatsirani pano pa tsamba lathu chifukwa simudzakhalanso mu mdima wa chilungamo.

Category